| |
Yes!
MALAWI
Let’s Pray! |
|
|
Inde!
Malawi
Tiyeni Tipemphere! |
|
|
|
 |
GOVERNMENT |
|
 |
BOMA |
|
| |
For the president and government to govern wisely & justly with integrity and without corruption, greed or the need for personal power. |
|
|
Pulezidenti ndi boma kuti alamulire mwa chidziwitso, chilungamo ndi nzeru mopanda dyera, ziphuphu kapena kudzikundikira / kumphangira mphavu / ulamuliro.
|
|
| |
THE CHURCH |
|
|
MPINGO |
|
| |
For brokenness and humility in the church to pray more and build God’s Kingdom together in all of Malawi. |
|
|
Upemphere kwambiri, mosweka mtima ndi kudzichepetsa ndi kumanga ufumu wa Mulungu mu dziko lathu lino la Malawi.
|
|
|
|
 |
GOD'S FAVOR |
|
 |
KUKONDEREDWA NDI MULUNGU
|
|
| |
For God’s favor, grace and blessing unto Malawi! |
|
|
Mulungu atikondere, kutikhululukira ndi kudalitsa dziko lino la Malawi.
|
|
| |
FAMILIES |
|
|
MABANJA |
|
| |
For strong united families with faithful fathers who love and care for their families. |
|
|
Mabanja olimba, okondana okhulupilirana komanso woyan ganira bwino ma banja awo.
|
|
|
|
 |
EDUCATION |
|
 |
MAPHUNZIRO |
|
| |
For the best education to become more available to all Malawians. |
|
|
Maphunziro a pamwambe apezeke kwa a Malawi onse.
|
|
| |
DEVELOPMENT AND ECONOMY |
|
|
CHITUKUKO NDI CHUMA |
|
| |
For honest, Godly business practice and profitable contracts to develop the economy and create more job opportunities. That people will work very hard. For research breakthroughs to improve development. |
|
|
Mabizinezi achitike mwa chilungamo ndi mowopa Mulungu kuti phindu lake litukule chuma chadziko lino komanso kuti anthu ambiri apeze mwai wa ntchito. Anthu azigwira ntchito molimbikira. Kuboleza pakafukufuku wopititsa chitukuko patsogolo. |
|
|
|
 |
INTERNATIONAL RELATIONS |
|
 |
UBALE NDI MAYIKO ENA |
|
| |
That only people and nations with good motives towards Malawi will succeed to visit and work with the Malawian government & its people. |
|
|
Anthu ndi mayiko okhawo omwe ali ndi zolinga zabwino aziloledwa kubwera ndi kudzagwira ntchito ndi boma lathu lino komanso athu.
|
|
| |
HEALTHCARE |
|
|
CHISAMALIRO CHA ZAUMAYO |
|
| |
The establishment of nationwide affordable healthcare for everyone as well as very good healthcare education so
Malawians can prevent diseases through healthy lifestyle. |
|
|
Zipatala zimangidwe m’madera onse a dziko lino ndikuti mankhwala azipezeka pa mtengo wabwino. A Malawi aphunzitsidwe za o moyo kuti azitha kupewa matenda. |
|
|
|
 |
MENTALITY AND MINDSETS |
|
 |
MAGANIZO NDI MALINGALIRO |
|
| |
That mindsets will change and people will believe and
expect that “All things are possible with God and through
His ways!” For a better future for all. |
|
|
Kuti tikhale ndi tsogolo la bwino, maganizo Ndi malingaliro a anthu asithe ndipo azikhulupilira kuti zonse ndi zotheka ndi Mulungu pakutsatira njira za Mulungu.
|
|
| |
COMMUNICATIONS AND MEDIA |
|
|
MAUTHENGA |
|
| |
That only the Truth will be communicated with Godly wisdom on TV, radio, media and the like. |
|
|
Uthenga woperekedwa kwa anthu kupyolera pa kanema, wailesi ndi nyuzipepala uzikhala wa choonadi ndipo uziperekedwa mwa nzero ndi kuopa Mulungu. |
|
|
|
 |
|
|
 |
|
| |
Repent! Worship and thank God. Evaluate your culture and ways against God’s Word. Do good to your
family & others! |
|
|
Lapani! Lambirani ndi kuthokoza
Mulungu! Unguzani khalidwe ndi ngira zanu ngati zikufanana ndi mau a Mulungu. Kuchitira zabwino anthu ena!
|
|
| |
BUILDING MALAWI ON THE ROCK! |
|
|
TIMANGE MALAWI PA TANTHWE! |
|
| |
"Therefore everyone who hears these words of mine and puts them into practice is like a wise man who built his house on the rock. The rain came down, the streams rose, and the wind blew and beat against that house, yet it did not fall, because it had its foundation on the rock.”
(Matt 7:24-25) |
|
|
“Chomwhecho iye wakumva mau anga ndi kuwawachita ali ngati munthu wazeru amene wamanga nyumba yake pathandwe. Mvula ingawa, misinje nadzadza, Mphepo yankuntho naiomba koma wosagwa. Chifukwa inamangidwa pa tanthwe.” (Mateyu 7:24-25)
|
|
| |
|
|
|
|
|
| |
Provided compliments of RockAfrica in partnership with Y-Malawi |
|